Anthu ambili atutumuka pamene dziko la Iran yabwenza kuphulisa ku America,
Dziko la Iran lapanga chinthu chimene anthu sanayembekedzele kuti lingachite pobwenzela chiwembu chimene dziko la America linachita. A Trump anazitamilira dzulo pamasamba awo a mchezo komanso pa TV kuti akaphulisa ku dziko la Iran ngati njila yofuna kuopyezela dzikoli kuti lisiye nkhondo yophulitsana yomwe Iran inayambitsa ku dziko la Israel.
Kotelo a Trump anaopyeza so dziko la Iran kuti akapitiliza nkhondo komanso kuphulitsa dziko la Israel, America ipitiliza kukaphulitsa ku Iran. Koma chomwe chadabwitsa, Mmalo mwake dziko la Iran layankha mwa changu pa chiwembu chi opanda mantha pokaphulisa ku bwalo lina la asilikali ku America konko.
Tikunena pano zikumveka kuti president yu wapitisidwa kale ku zipinda zotetezeka zomwe zimakonzedwa kuti akabisale nthawi imene kuli chiopyezo cha chiwembu. Anthu sanayembekedzele kuti dziko ngati Iran ingapange attack dziko la America kutengela kuti ndi dziko lomwe ambili amaliopa.
Iran yi apapa yaonesa kulimba mtima kopitilila mulingo, moti pali chiopyezo chokuti kutha kubuka nkhondo yaikulu kuchokera apapa. Ndipo dziko la Iran yaopyzanso kuti lipha asilikali okwana 50,000 aku America ngati zowaopyeza zitapitilire.
Akulu akulu a nkhondo aku Iran akuti America isiye kulowelera Zinthu zokuti sizikuwakhuza, ndiye nawo akuti iyi so ndi warning kuti America iphunzile kupanga zake. Kwavuta
Maso ali kufuna kumva Trump ayankha motani izi
DZikomo potidziwitsa zamaiko ndpo takunyadilan pitilidzan ku telo 0994325728
Claim
Claim